-
Mateyu 22:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho pitani mʼmisewu yotulukira mumzinda ndipo aliyense amene mukamupeze, mukamuitane kuti abwere kuphwando laukwatili.’+ 10 Ndiyeno akapolowo anapita mʼmisewu ndipo anasonkhanitsa onse amene anawapeza, oipa ndi abwino omwe. Ndipo chipinda chodyeramo phwando laukwati chinadzaza ndi anthu amene ankadya chakudya.
-