Mateyu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira.+ Maliko 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako iye anaitana gulu la anthu limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira.+ Luka 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira tsiku ndi tsiku.+
24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira.+
34 Kenako iye anaitana gulu la anthu limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira.+
23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndipo anyamule mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira tsiku ndi tsiku.+