-
Luka 24:25-27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno iye anawauza kuti: “Opanda nzeru inu komanso okayikakayika pa zinthu zonse zimene aneneri ananena! 26 Kodi sikunali koyenera kuti Khristu amve zowawa zonsezi+ nʼkulowa mu ulemerero wake?”+ 27 Atatero anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo mʼMalemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose komanso zonse zimene aneneri analemba.+
-