21 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, ngati mutakhala ndi chikhulupiriro ndipo simukukayikira, mudzatha kuchita zimene ndachitira mkuyu umenewu. Komanso kuposa pamenepa, mudzatha kuuza phiri ili kuti, ‘Nyamuka pano ukadziponye mʼnyanja,’ ndipo zidzachitikadi.+