Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+ Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+
5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+
16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+