Yohane 6:67, 68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndiyeno Yesu anafunsa ophunzira ake 12 aja kuti: “Inunso mukufuna kupita kapena?” 68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+
67 Ndiyeno Yesu anafunsa ophunzira ake 12 aja kuti: “Inunso mukufuna kupita kapena?” 68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+