Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+ Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mʼmawa kutacha, ansembe aakulu onse limodzi ndi akulu a anthu anakambirana nʼkugwirizana kuti aphe Yesu.+ Maliko 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+ Machitidwe 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafumu a dziko lapansi anaima pamalo awo, ndipo olamulira anasonkhana mogwirizana kuti alimbane ndi Yehova* komanso wodzozedwa* wake.’+
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+
27 Mʼmawa kutacha, ansembe aakulu onse limodzi ndi akulu a anthu anakambirana nʼkugwirizana kuti aphe Yesu.+
15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+
26 Mafumu a dziko lapansi anaima pamalo awo, ndipo olamulira anasonkhana mogwirizana kuti alimbane ndi Yehova* komanso wodzozedwa* wake.’+