Mateyu 27:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kuyambira cha mʼma 12 koloko masana* kunagwa mdima mʼdziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+ Maliko 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi itakwana cha mʼma 12 koloko masana* kunagwa mdima mʼdziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+
33 Nthawi itakwana cha mʼma 12 koloko masana* kunagwa mdima mʼdziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+