Mateyu 27:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+ Maliko 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya mayi wa Yose, anapitiriza kuyangʼanitsitsa pamene anaikidwapo.+
61 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+
47 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya mayi wa Yose, anapitiriza kuyangʼanitsitsa pamene anaikidwapo.+