14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi la nyama+ ndipo ankakhala pakati pathu. Ife tinaona ulemerero wake, ulemerero wofanana ndi umene mwana wobadwa yekha+ amalandira kuchokera kwa bambo ake. Mulungu ankamukomera mtima kwambiri komanso ankaphunzitsa choonadi.