Mateyu 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Inde, pali zinthu zambiri zofunika kukolola, koma antchito ndi ochepa.+
37 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Inde, pali zinthu zambiri zofunika kukolola, koma antchito ndi ochepa.+