Yohane 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tiyenera kugwira ntchito za Mulungu amene anandituma kudakali masana.+ Usiku ukubwera pamene munthu sangagwire ntchito. Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.
4 Tiyenera kugwira ntchito za Mulungu amene anandituma kudakali masana.+ Usiku ukubwera pamene munthu sangagwire ntchito.
10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.