-
2 Mafumu 4:32-34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Elisa atalowa mʼnyumbamo, anapeza mwana wakufayo atamʼgoneka pabedi lake lija.+ 33 Ndiyeno analowa kuchipinda nʼkutseka chitseko ndipo analiko awiriwiri. Atatero anayamba kupemphera kwa Yehova.+ 34 Kenako anapita pabedipo ndipo anagwada nʼkuweramira mwanayo. Anagunditsa pakamwa pake ndi pakamwa pa mwanayo, maso ake ndi maso a mwanayo komanso manja ake ndi manja a mwanayo. Anakhalabe choncho mpaka thupi la mwanayo linayamba kutentha.+
-