Yohane 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atate saweruza munthu aliyense, koma wapereka udindo wonse woweruza kwa Mwana,+ 2 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu, amene adzaweruze+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ ndiponso akadzabwera mu Ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti:
4 Pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu, amene adzaweruze+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ ndiponso akadzabwera mu Ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti: