Mateyu 11:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Bwerani kwa ine inu nonse amene mukugwira ntchito yotopetsa ndi olemedwa ndipo ndidzakutsitsimulani. 29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa. Yohane 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu amene munawatenga mʼdziko nʼkundipatsa, ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine ndipo iwo amvera mawu anu.
28 Bwerani kwa ine inu nonse amene mukugwira ntchito yotopetsa ndi olemedwa ndipo ndidzakutsitsimulani. 29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa.
6 Anthu amene munawatenga mʼdziko nʼkundipatsa, ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine ndipo iwo amvera mawu anu.