23 Iye anapitiriza kuwauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano koma ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera mʼdziko lino koma ine si wochokera mʼdziko lino.
42 Yesu anawauza kuti: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ chifukwa ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano. Sindinabwere mwakufuna kwanga koma Iyeyo ndi amene anandituma.+