51 Tamverani, ndikuuzeni chinsinsi chopatulika: Sikuti tonse tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasintha,+ 52 mʼkanthawi kochepa, mʼkuphethira kwa diso, pa kulira kwa lipenga lomaliza. Chifukwa lipenga lidzalira,+ kenako akufa adzaukitsidwa ndi matupi oti sangawonongeke ndipo tidzasintha.