Yohane 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anzanga apamtima inu,* ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo mogwirizana ndi zimene ndinauza Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo. Yohane 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa kanthawi simudzandionanso,+ ndipo kwa kanthawi mudzandiona.”
33 Anzanga apamtima inu,* ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo mogwirizana ndi zimene ndinauza Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo.