16 Patapita nthawi, Yehova anauza Samueli kuti: “Kodi ulirira Sauli mpaka liti,+ munthu woti ine ndamukana kuti akhale mfumu ya Isiraeli?+ Thira mafuta mʼnyanga yako+ ndipo unyamuke. Ndikutumiza kwa Jese+ wa ku Betelehemu, chifukwa ndasankha mmodzi wa ana ake aamuna kuti akhale mfumu yanga.”+