Mateyu 7:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+ 29 chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu waulamuliro,+ osati ngati alembi awo. Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+
28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+ 29 chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu waulamuliro,+ osati ngati alembi awo.
22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+