Yohane 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu nʼkupereka chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona, moti zimene ndinamva kwa iye ndi zimene ndikuzilankhula mʼdzikoli.”+
26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu nʼkupereka chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona, moti zimene ndinamva kwa iye ndi zimene ndikuzilankhula mʼdzikoli.”+