Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+ Yohane 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha anzake.+ 1 Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tadziwa chikondi chifukwa chakuti Yesu Khristu anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+
28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+
13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha anzake.+
16 Tadziwa chikondi chifukwa chakuti Yesu Khristu anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+