Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+ Ezekieli 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+ 1 Petulo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo mʼbusa wamkulu+ akadzaonekera, mudzalandira mphoto* yosawonongeka yomwe ndi yaulemerero.+
23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+
24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+