19 Kenako analamula gulu la anthulo kuti likhale pansi pa udzu. Ndiyeno anatenga mitanda ya mkate 5 ndi nsomba ziwiri zija nʼkuyangʼana kumwamba ndi kupemphera.+ Atatero ananyemanyema mitanda ya mkate ija nʼkuipereka kwa ophunzirawo ndipo iwo anagawira gulu la anthulo.