Mateyu 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva chisoni* chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+ Maliko 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva* chisoni+ chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+
38 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva chisoni* chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+
34 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva* chisoni+ chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+