Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Amene wakulandirani walandiranso ine ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Maliko 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Aliyense amene walandira mwana wamngʼono+ ngati ameneyu mʼdzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense amene walandira ine, sanalandire ine ndekha, koma walandiranso Mulungu amene anandituma.”+
37 “Aliyense amene walandira mwana wamngʼono+ ngati ameneyu mʼdzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense amene walandira ine, sanalandire ine ndekha, koma walandiranso Mulungu amene anandituma.”+