-
1 Atesalonika 4:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Chifukwa Ambuyewo adzatsika kuchoka kumwamba ndi mfuu yolamula. Mawu awo adzamveka kuti ndi a mkulu wa angelo+ ndipo adzanyamula lipenga la Mulungu mʼdzanja lawo. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka.+ 17 Pambuyo pake ife amene tidzakhale tidakali ndi moyo, limodzi ndi iwowo, tidzatengedwa kupita mʼmitambo+ kukakumana ndi Ambuye+ mumlengalenga ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+
-