-
Afilipi 4:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+ 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene anthu sangathe kuumvetsa, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu pamene mukutsatira Khristu Yesu.
-