2 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukamachita zinthu zonsezi komanso mukamasonyeza kwambiri makhalidwewa, mudzagwiritsa ntchito zinthu zimene mukuzidziwa molondola zokhudza Ambuye wathu Yesu Khristu ndipo zidzakuthandizani kuti musamangokhala kapena kulephera kubereka zipatso.+
8 Mukamachita zinthu zonsezi komanso mukamasonyeza kwambiri makhalidwewa, mudzagwiritsa ntchito zinthu zimene mukuzidziwa molondola zokhudza Ambuye wathu Yesu Khristu ndipo zidzakuthandizani kuti musamangokhala kapena kulephera kubereka zipatso.+