Akolose 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatipulumutsa ku ulamuliro wa mdima,+ nʼkutisamutsira mu ufumu wa Mwana wake wokondedwa.