Yohane 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamuweruze nokha mogwirizana ndi chilamulo chanu.”+ Ayudawo anamuuza kuti: “Tilibe ulamuliro wopha munthu aliyense.”+
31 Ndiyeno Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamuweruze nokha mogwirizana ndi chilamulo chanu.”+ Ayudawo anamuuza kuti: “Tilibe ulamuliro wopha munthu aliyense.”+