Levitiko 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho munthu amene wanyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Gulu lonse lizimuponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.
16 Choncho munthu amene wanyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Gulu lonse lizimuponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.