31 Popeza linali Tsiku Lokonzekera,+ Ayudawo sanafune kuti mitembo ikhalebe pamitengo yozunzikirapo+ tsiku la Sabata, (chifukwa Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu),+ ndiye iwo anapempha Pilato kuti awalole kuti athyole miyendo ya anthu amene anapachikidwawo nʼkutsitsa mitembo yawo.