Yohane 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mmodzi wa ophunzirawo, amene Yesu ankamukonda,+ anakhala pafupi ndi Yesu.* Yohane 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Yesu ataona mayi akewo ndi wophunzira amene ankamukonda uja+ ataima chapafupi, anauza mayi akewo kuti: “Mayi, kuyambira lero, uyu akhala mwana wanu.” Yohane 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anathamanga kupita kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina, amene Yesu ankamukonda kwambiri uja.+ Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa mʼmanda*+ muja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.” Yohane 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, wophunzira amene Yesu ankamukonda kwambiri uja+ anauza Petulo kuti: “Ndi Ambuye!” Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake akunja, chifukwa anali maliseche,* ndipo analumphira mʼnyanja.
26 Choncho Yesu ataona mayi akewo ndi wophunzira amene ankamukonda uja+ ataima chapafupi, anauza mayi akewo kuti: “Mayi, kuyambira lero, uyu akhala mwana wanu.”
2 Choncho anathamanga kupita kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina, amene Yesu ankamukonda kwambiri uja.+ Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa mʼmanda*+ muja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.”
7 Zitatero, wophunzira amene Yesu ankamukonda kwambiri uja+ anauza Petulo kuti: “Ndi Ambuye!” Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake akunja, chifukwa anali maliseche,* ndipo analumphira mʼnyanja.