Yohane 1:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yohane anapereka umboni pamene Ayuda anatumiza ansembe ndi Alevi kuchokera ku Yerusalemu kukamufunsa kuti: “Kodi ndiwe ndani?”+ 20 Iye anavomera ndipo sanakane. Ananena kuti: “Ine si Khristu.”
19 Yohane anapereka umboni pamene Ayuda anatumiza ansembe ndi Alevi kuchokera ku Yerusalemu kukamufunsa kuti: “Kodi ndiwe ndani?”+ 20 Iye anavomera ndipo sanakane. Ananena kuti: “Ine si Khristu.”