Yohane 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anapitiriza kuwauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano koma ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera mʼdziko lino koma ine si wochokera mʼdziko lino.
23 Iye anapitiriza kuwauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano koma ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera mʼdziko lino koma ine si wochokera mʼdziko lino.