-
Machitidwe 17:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma anthu ena anzeru za Epikureya ndi Sitoiki anayamba kutsutsana naye. Ena ankanena kuti: “Kodi nayenso wobwetuka uyu akufuna kunena chiyani?” Pomwe ena ankanena kuti: “Akuoneka kuti akulalikira za milungu yachilendo.” Ankanena zimenezi chifukwa chakuti Paulo ankalengeza uthenga wabwino wa Yesu ndi za kuuka kwa akufa.+
-