Machitidwe 2:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Anthu onse anayamba kuchita mantha kwambiri ndipo atumwiwo anayamba kuchita zinthu zodabwitsa ndiponso zizindikiro zambiri.+ Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndiponso zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse ankasonkhana Pakhonde la Zipilala la Solomo.+
43 Anthu onse anayamba kuchita mantha kwambiri ndipo atumwiwo anayamba kuchita zinthu zodabwitsa ndiponso zizindikiro zambiri.+
12 Atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndiponso zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse ankasonkhana Pakhonde la Zipilala la Solomo.+