17 Ngati mungatiponyere mungʼanjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye akhozanso kutipulumutsa mʼmanja mwanu mfumu.+ 18 Koma ngakhale atapanda kutipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu kapena kulambira fano lagolide limene mwaimika.”+