Genesis 49:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yakobo atamaliza kupereka malangizo kwa ana akewo, anabwezeranso miyendo yake pabedi, nʼkumwalira. Kenako anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.*+ Ekisodo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi Yosefe anamwalira,+ chimodzimodzinso abale ake onse ndi anthu a mʼbadwo wonsewo.
33 Yakobo atamaliza kupereka malangizo kwa ana akewo, anabwezeranso miyendo yake pabedi, nʼkumwalira. Kenako anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.*+