-
Ekisodo 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tiyeni tiwachenjerere anthu amenewa kuti asapitirize kuchulukana, kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu nʼkumenyana nafe kenako nʼkuchoka mʼdziko muno.”
-