Ekisodo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wamkazi wa Farao atapita kukasamba mumtsinje wa Nailo, atsikana ake omutumikira ankayenda mʼmphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabasiketi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+ Ekisodo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+
5 Mwana wamkazi wa Farao atapita kukasamba mumtsinje wa Nailo, atsikana ake omutumikira ankayenda mʼmphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabasiketi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+
10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+