Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Angelo onse ndi mizimu yotumikira ena.*+ Mulungu amawatumiza kuti akatumikire omwe iye adzawapulumutse. Chivumbulutso 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinaona mngelo wina akuuluka chapafupi mumlengalenga. Iye anali ndi uthenga wabwino wosatha woti aulengeze kwa anthu amene akukhala padziko lapansi, kudziko lililonse, fuko lililonse, chilankhulo chilichonse ndi mtundu uliwonse.+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+
14 Angelo onse ndi mizimu yotumikira ena.*+ Mulungu amawatumiza kuti akatumikire omwe iye adzawapulumutse.
6 Ndinaona mngelo wina akuuluka chapafupi mumlengalenga. Iye anali ndi uthenga wabwino wosatha woti aulengeze kwa anthu amene akukhala padziko lapansi, kudziko lililonse, fuko lililonse, chilankhulo chilichonse ndi mtundu uliwonse.+