Mateyu 10:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina ndipo musalowe mumzinda uliwonse wa Asamariya.+ 6 Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+
5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina ndipo musalowe mumzinda uliwonse wa Asamariya.+ 6 Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+