Mateyu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana.+
7 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana.+