Machitidwe 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika mumzinda wa Salami anayamba kulalikira mawu a Mulungu mʼmasunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane yemwe ankawatumikira.*+ Machitidwe 15:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Baranaba ankafunitsitsa kuti atenge Yohane, wotchedwanso Maliko.+ 38 Koma Paulo anaona kuti si bwino kumutenga chifukwa ulendo wina Yohane anawasiya ku Pamfuliya ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.+
5 Atafika mumzinda wa Salami anayamba kulalikira mawu a Mulungu mʼmasunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane yemwe ankawatumikira.*+
37 Baranaba ankafunitsitsa kuti atenge Yohane, wotchedwanso Maliko.+ 38 Koma Paulo anaona kuti si bwino kumutenga chifukwa ulendo wina Yohane anawasiya ku Pamfuliya ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.+