1 Samueli 8:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Patapita nthawi, akulu onse a mu Isiraeli anasonkhana pamodzi nʼkupita kwa Samueli ku Rama. 5 Iwo anamuuza kuti: “Inuyo mwakalamba, koma ana anu sakutsatira chitsanzo chanu. Ndiye mutisankhire mfumu yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”+
4 Patapita nthawi, akulu onse a mu Isiraeli anasonkhana pamodzi nʼkupita kwa Samueli ku Rama. 5 Iwo anamuuza kuti: “Inuyo mwakalamba, koma ana anu sakutsatira chitsanzo chanu. Ndiye mutisankhire mfumu yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”+