Mateyu 28:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mngeloyo anauza azimayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo.+ 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona. Machitidwe 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mulungu anamuukitsa+ pomumasula ku zopweteka* za imfa, chifukwa zinali zosatheka kuti imfa imugwire mwamphamvu.+
5 Koma mngeloyo anauza azimayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo.+ 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona.
24 Koma Mulungu anamuukitsa+ pomumasula ku zopweteka* za imfa, chifukwa zinali zosatheka kuti imfa imugwire mwamphamvu.+