Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa simudzandisiya* mʼManda.*+ Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.*+ Machitidwe 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anadziwiratu zamʼtsogolo ndipo ananeneratu za kuuka kwa Khristu kuti sanasiyidwe mʼManda,* komanso thupi lake silinavunde.+
31 Iye anadziwiratu zamʼtsogolo ndipo ananeneratu za kuuka kwa Khristu kuti sanasiyidwe mʼManda,* komanso thupi lake silinavunde.+