Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+ Machitidwe 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zimenezi,+ chimodzimodzinso mzimu woyera,+ umene Mulungu wapereka kwa anthu amene amamumvera monga wolamulira.”
13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
32 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zimenezi,+ chimodzimodzinso mzimu woyera,+ umene Mulungu wapereka kwa anthu amene amamumvera monga wolamulira.”